1 Mafumu 8:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Akulu onse a Isiraeli anabwera, ndipo ansembe anayamba kunyamula+ Likasa.+