1 Mafumu 8:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 inuyo mumve muli kumwamba ndipo mukhululuke tchimo la anthu anu Aisiraeli,+ ndi kuwabwezeretsa+ kudziko limene munapatsa makolo awo.+
34 inuyo mumve muli kumwamba ndipo mukhululuke tchimo la anthu anu Aisiraeli,+ ndi kuwabwezeretsa+ kudziko limene munapatsa makolo awo.+