1 Mafumu 9:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ndipo Yehova anamuuza kuti: “Ndamva pemphero lako+ ndi pempho lako lopempha chifundo kwa ine. Ndayeretsa+ nyumba imene wamangayi mwa kuikapo dzina langa+ mpaka kalekale, ndipo maso anga+ ndi mtima wanga adzakhala pamenepo nthawi zonse.+
3 Ndipo Yehova anamuuza kuti: “Ndamva pemphero lako+ ndi pempho lako lopempha chifundo kwa ine. Ndayeretsa+ nyumba imene wamangayi mwa kuikapo dzina langa+ mpaka kalekale, ndipo maso anga+ ndi mtima wanga adzakhala pamenepo nthawi zonse.+