1 Mafumu 11:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 koma sindidzauchotsa wonse.+ Ndidzapereka fuko limodzi kwa mwana wako, chifukwa cha Davide mtumiki wanga+ ndiponso chifukwa cha Yerusalemu, mzinda umene ndausankha.”+
13 koma sindidzauchotsa wonse.+ Ndidzapereka fuko limodzi kwa mwana wako, chifukwa cha Davide mtumiki wanga+ ndiponso chifukwa cha Yerusalemu, mzinda umene ndausankha.”+