1 Mafumu 12:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Yerobowamu anapereka nsembe pa tsiku la 15, m’mwezi wa 8 womwe anausankha yekha.+ Anapereka nsembezo paguwa limene anamanga ku Beteli. Ndipo anakonzera chikondwerero ana a Isiraeli ndi kupereka nsembe zautsi kuti afukize paguwalo.+
33 Yerobowamu anapereka nsembe pa tsiku la 15, m’mwezi wa 8 womwe anausankha yekha.+ Anapereka nsembezo paguwa limene anamanga ku Beteli. Ndipo anakonzera chikondwerero ana a Isiraeli ndi kupereka nsembe zautsi kuti afukize paguwalo.+