1 Mafumu 14:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Yehova anali atauza Ahiya kuti: “Kukubwera mkazi wa Yerobowamu kudzakufunsa za mwana wake, chifukwa mwanayo akudwala. Umuuze zakutizakuti. Zomwe zichitike n’zakuti, akangofika adzisintha kuti asadziwike.”+
5 Yehova anali atauza Ahiya kuti: “Kukubwera mkazi wa Yerobowamu kudzakufunsa za mwana wake, chifukwa mwanayo akudwala. Umuuze zakutizakuti. Zomwe zichitike n’zakuti, akangofika adzisintha kuti asadziwike.”+