-
1 Mafumu 18:25Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
25 Tsopano Eliya anauza aneneri a Baala kuti: “Yambani ndinu kusankha ng’ombe yaing’ono yamphongo imodzi ndi kuikonza, chifukwa mulipo ambiri. Muitane dzina la mulungu wanu koma musayatse moto.”
-