1 Mafumu 18:42 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 42 Ahabu anapitadi kukadya ndi kukamwa. Koma Eliya anapita pamwamba pa phiri la Karimeli. Ndiyeno anakhala chogwada+ ataika nkhope yake pakati pa mawondo ake.+ 1 Mafumu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 18:42 Tsanzirani, ptsa. 93-94 Nsanja ya Olonda,4/1/2008, ptsa. 17-18
42 Ahabu anapitadi kukadya ndi kukamwa. Koma Eliya anapita pamwamba pa phiri la Karimeli. Ndiyeno anakhala chogwada+ ataika nkhope yake pakati pa mawondo ake.+