1 Mafumu 19:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Eliya atangomva mawuwo, nthawi yomweyo anaphimba nkhope yake ndi chovala chake,+ ndipo anatuluka kukaima pakhomo la phangalo. Pamenepo panamveka mawu olankhula naye, ndipo mawuwo anam’funsa kuti: “Ukufuna chiyani kuno Eliya?”+
13 Eliya atangomva mawuwo, nthawi yomweyo anaphimba nkhope yake ndi chovala chake,+ ndipo anatuluka kukaima pakhomo la phangalo. Pamenepo panamveka mawu olankhula naye, ndipo mawuwo anam’funsa kuti: “Ukufuna chiyani kuno Eliya?”+