2 Mafumu 18:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Musalole kuti Hezekiya akuchititseni kudalira Yehova,+ pokuuzani kuti: “Mosakayikira Yehova atilanditsa,+ ndipo mzindawu superekedwa m’manja mwa mfumu ya Asuri.”+
30 Musalole kuti Hezekiya akuchititseni kudalira Yehova,+ pokuuzani kuti: “Mosakayikira Yehova atilanditsa,+ ndipo mzindawu superekedwa m’manja mwa mfumu ya Asuri.”+