2 Mafumu 18:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Musamvere Hezekiya chifukwa mfumu ya Asuri yanena kuti: “Ndigonjereni, ndipo bwerani kwa ine. Aliyense azidya zochokera mumtengo wake wa mpesa ndi mumtengo wake wa mkuyu,+ komanso aliyense azimwa madzi a m’chitsime chake,+
31 Musamvere Hezekiya chifukwa mfumu ya Asuri yanena kuti: “Ndigonjereni, ndipo bwerani kwa ine. Aliyense azidya zochokera mumtengo wake wa mpesa ndi mumtengo wake wa mkuyu,+ komanso aliyense azimwa madzi a m’chitsime chake,+