2 Mafumu 19:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Anthu a nyumba ya Yuda amene adzapulumuke, amene adzatsale,+ ndithu adzazika mizu pansi n’kubereka zipatso m’mwamba.+
30 Anthu a nyumba ya Yuda amene adzapulumuke, amene adzatsale,+ ndithu adzazika mizu pansi n’kubereka zipatso m’mwamba.+