2 Mafumu 21:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Pomalizira pake, Manase anagona pamodzi ndi makolo ake+ ndipo anaikidwa m’manda m’munda wa panyumba pake, m’munda wa Uziza.+ Kenako Amoni mwana wake anayamba kulamulira m’malo mwake.
18 Pomalizira pake, Manase anagona pamodzi ndi makolo ake+ ndipo anaikidwa m’manda m’munda wa panyumba pake, m’munda wa Uziza.+ Kenako Amoni mwana wake anayamba kulamulira m’malo mwake.