2 Mafumu 22:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Tsopano Safani mlembi anapita kwa mfumu n’kuiuza kuti: “Atumiki anu akhuthula ndalama zimene anazipeza m’nyumbayo, ndipo akuzipereka kwa ogwira ntchito osankhidwa a m’nyumba ya Yehova.”+
9 Tsopano Safani mlembi anapita kwa mfumu n’kuiuza kuti: “Atumiki anu akhuthula ndalama zimene anazipeza m’nyumbayo, ndipo akuzipereka kwa ogwira ntchito osankhidwa a m’nyumba ya Yehova.”+