2 Mafumu 25:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ena mwa anthu onyozeka+ a m’dzikolo, mkulu wa asilikali olondera mfumu uja anawasiya kuti akhale olima minda ya mpesa ndi alimi ogwira ntchito mokakamizidwa.+
12 Ena mwa anthu onyozeka+ a m’dzikolo, mkulu wa asilikali olondera mfumu uja anawasiya kuti akhale olima minda ya mpesa ndi alimi ogwira ntchito mokakamizidwa.+