-
2 Mafumu 25:19Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
19 Mumzindawo anatengamo nduna imodzi ya panyumba ya mfumu imene inali kuyang’anira amuna ankhondo. Anatenganso amuna asanu kuchokera pa anthu amene ankatha kuonana ndi mfumu mwa amuna amene anali mumzindamo. Komanso anatenga mlembi wa mkulu wa asilikali yemwe anali kusonkhanitsa ankhondo a m’dzikolo, ndi amuna 60 mwa anthu a m’dzikolo amene anali mumzindawo.+
-