2 Mafumu 4:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Elisa anati: “Ndiye timuchitire chiyani?” Gehazi anayankha kuti: “Mayiyutu alibe mwana wamwamuna,+ ndipo mwamuna wake ndi wokalamba.”
14 Elisa anati: “Ndiye timuchitire chiyani?” Gehazi anayankha kuti: “Mayiyutu alibe mwana wamwamuna,+ ndipo mwamuna wake ndi wokalamba.”