2 Mafumu 4:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Ndiyeno Elisa anati: “Chaka chamawa nthawi ngati yomwe ino mudzakhala mukuyangata mwana wamwamuna.”+ Koma mayiyo atamva anati: “Iyayi mbuyanga, munthu wa Mulungu woona! Musandinamize ine kapolo wanu.”
16 Ndiyeno Elisa anati: “Chaka chamawa nthawi ngati yomwe ino mudzakhala mukuyangata mwana wamwamuna.”+ Koma mayiyo atamva anati: “Iyayi mbuyanga, munthu wa Mulungu woona! Musandinamize ine kapolo wanu.”