2 Mafumu 4:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Wantchitoyo ananyamuladi mwanayo n’kupita naye kwa mayi ake. Mayi akewo anamukhazika pamwendo mpaka masana, kenako mwanayo anamwalira.+
20 Wantchitoyo ananyamuladi mwanayo n’kupita naye kwa mayi ake. Mayi akewo anamukhazika pamwendo mpaka masana, kenako mwanayo anamwalira.+