2 Mafumu 4:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Chotero mayiyo anayenda n’kukafika kwa munthu wa Mulungu woona uja paphiri la Karimeli. Munthu wa Mulungu woonayo ataona mayiyo chapatali, anauza mtumiki wake Gehazi kuti:+ “Taona, mayi wachisunemu uja uyo!
25 Chotero mayiyo anayenda n’kukafika kwa munthu wa Mulungu woona uja paphiri la Karimeli. Munthu wa Mulungu woonayo ataona mayiyo chapatali, anauza mtumiki wake Gehazi kuti:+ “Taona, mayi wachisunemu uja uyo!