2 Mafumu 5:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Tsopano atumiki ake anamutsatira ndipo anamufunsa kuti: “Bambo wanga,+ kodi mneneriyo akanakuuzani kuti muchite chinthu chachikulu, simukanachita? Nanga bwanji poti wangokuuzani kuti, ‘Kasambeni ndi kuyeretsedwa’?”
13 Tsopano atumiki ake anamutsatira ndipo anamufunsa kuti: “Bambo wanga,+ kodi mneneriyo akanakuuzani kuti muchite chinthu chachikulu, simukanachita? Nanga bwanji poti wangokuuzani kuti, ‘Kasambeni ndi kuyeretsedwa’?”