2 Mafumu 5:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Namani atamva zimenezi, anatsetserekera ku Yorodano n’kukamira maulendo 7, mogwirizana ndi mawu a munthu wa Mulungu woona+ uja. Pambuyo pake, mnofu wake unabwerera mwakale moti unakhala ngati mnofu wa kamnyamata,+ ndipo anakhala woyera.+
14 Namani atamva zimenezi, anatsetserekera ku Yorodano n’kukamira maulendo 7, mogwirizana ndi mawu a munthu wa Mulungu woona+ uja. Pambuyo pake, mnofu wake unabwerera mwakale moti unakhala ngati mnofu wa kamnyamata,+ ndipo anakhala woyera.+