2 Mafumu 5:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Pamenepo Namani anamuuza kuti: “Chabwino. Tenga matalente awiri.” Anamuumiriza+ mpaka anam’mangira matalente awiri a siliva m’matumba awiri, ndi zovala ziwiri. Anapereka zinthuzo kwa atumiki ake awiri kuti am’nyamulire.
23 Pamenepo Namani anamuuza kuti: “Chabwino. Tenga matalente awiri.” Anamuumiriza+ mpaka anam’mangira matalente awiri a siliva m’matumba awiri, ndi zovala ziwiri. Anapereka zinthuzo kwa atumiki ake awiri kuti am’nyamulire.