2 Mafumu 6:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Ndiyeno mfumuyo inam’funsa kuti: “Vuto lako ndi lotani?” Mayiyo anayankha kuti: “Mayi uyu anandiuza kuti, ‘Bweretsa mwana wako timudye lero, ndipo mwana wanga timudya mawa.’+
28 Ndiyeno mfumuyo inam’funsa kuti: “Vuto lako ndi lotani?” Mayiyo anayankha kuti: “Mayi uyu anandiuza kuti, ‘Bweretsa mwana wako timudye lero, ndipo mwana wanga timudya mawa.’+