2 Mafumu 9:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Koma iwo anati: “Ayi ukunama! Tiuze zoona.” Pamenepo Yehu anati: “Munthu uja anandiuza zakutizakuti, ndipo anati, ‘Yehova wanena kuti: “Ndikukudzoza iwe kukhala mfumu ya Isiraeli.”’”+
12 Koma iwo anati: “Ayi ukunama! Tiuze zoona.” Pamenepo Yehu anati: “Munthu uja anandiuza zakutizakuti, ndipo anati, ‘Yehova wanena kuti: “Ndikukudzoza iwe kukhala mfumu ya Isiraeli.”’”+