15 Pambuyo pake, mfumu Yehoramu+ inabwerera ku Yezereeli+ kukachira zilonda zake zimene Asiriya anaivulaza pamene inali kumenyana ndi Hazaeli mfumu ya Siriya.+
Kenako Yehu anati: “Ngati mukugwirizana nazo,+ musalole aliyense kuthawa kutuluka mumzinda uno kuti akanene ku Yezereeli.”