2 Mafumu 13:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Kenako iye anauza mfumu ya Isiraeliyo kuti: “Gwirani utawo.” Mfumuyo inaugwiradi, ndipo Elisa anaika manja ake pamanja+ a mfumuyo.
16 Kenako iye anauza mfumu ya Isiraeliyo kuti: “Gwirani utawo.” Mfumuyo inaugwiradi, ndipo Elisa anaika manja ake pamanja+ a mfumuyo.