2 Mafumu 13:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Ndiyeno Yehoasi mwana wa Yehoahazi, analandanso kwa Beni-hadadi mwana wa Hazaeli, mizinda imene iye analanda Yehoahazi bambo ake pankhondo. Yehoasi anagonjetsa Beni-hadadi katatu, ndipo analandanso mizinda ya Isiraeli.+
25 Ndiyeno Yehoasi mwana wa Yehoahazi, analandanso kwa Beni-hadadi mwana wa Hazaeli, mizinda imene iye analanda Yehoahazi bambo ake pankhondo. Yehoasi anagonjetsa Beni-hadadi katatu, ndipo analandanso mizinda ya Isiraeli.+