16 Panali pa nthawi imeneyi pamene Menahemu anachoka ku Tiriza n’kupita kukaukira mzinda wa Tifisa, n’kupha anthu onse amene anali mmenemo. Anawononganso dera lozungulira mzindawo chifukwa anthu ake sanamutsegulire chipata, ndipo akazi onse apakati a mumzindawo anawatumbula.+