2 Mafumu 17:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 M’chaka cha 9 cha Hoshiya, mfumu ya Asuri inalanda Samariya+ n’kutenga Aisiraeli kupita nawo ku Asuri.+ Mfumuyo inakaika Aisiraeliwo ku Hala+ ndi ku Habori pafupi ndi mtsinje wa Gozani,+ ndiponso m’mizinda ya Amedi.+ 2 Mafumu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 17:6 Mawu a Mulungu, tsa. 47 Nsanja ya Olonda,2/15/1988, tsa. 27
6 M’chaka cha 9 cha Hoshiya, mfumu ya Asuri inalanda Samariya+ n’kutenga Aisiraeli kupita nawo ku Asuri.+ Mfumuyo inakaika Aisiraeliwo ku Hala+ ndi ku Habori pafupi ndi mtsinje wa Gozani,+ ndiponso m’mizinda ya Amedi.+