1 Mbiri 5:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Chifukwa chakuti Yuda+ anali wamphamvu pakati pa abale ake, mwa iye munachokera mtsogoleri,+ koma udindo wa woyamba kubadwa unali wa Yosefe.+ 1 Mbiri Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 5:2 Nsanja ya Olonda,10/1/2005, tsa. 9
2 Chifukwa chakuti Yuda+ anali wamphamvu pakati pa abale ake, mwa iye munachokera mtsogoleri,+ koma udindo wa woyamba kubadwa unali wa Yosefe.+