-
1 Mbiri 11:23Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
23 Benaya ndiye anaphanso Mwiguputo wa msinkhu waukulu modabwitsa, yemwe anali chiphona chachitali mikono* isanu.+ Mwiguputoyo anali ndi mkondo+ m’manja mwake, waukulu ngati mtanda wa owomba nsalu, koma Benaya anapitabe kukakumana naye atanyamula ndodo, n’kulanda mkondowo ndipo anamupha ndi mkondo wake womwewo.+
-