1 Mbiri 23:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Yahati anali mtsogoleri wawo, ndipo wachiwiri wake anali Ziza. Koma Yeusi ndi Beriya analibe ana ambiri aamuna, choncho anakhala nyumba imodzi ya makolo+ ndiponso gulu limodzi lokhala ndi udindo wofanana.
11 Yahati anali mtsogoleri wawo, ndipo wachiwiri wake anali Ziza. Koma Yeusi ndi Beriya analibe ana ambiri aamuna, choncho anakhala nyumba imodzi ya makolo+ ndiponso gulu limodzi lokhala ndi udindo wofanana.