11 Atatero, Davide anapatsa Solomo mwana wake mapulani akamangidwe+ ka khonde+ ndi nyumba zake, zipinda zake zosungiramo katundu,+ zipinda zake zakudenga,+ zipinda zake zamkati zosalowa kuwala kwambiri, ndi nyumba yokhalamo chivundikiro chophimba machimo.+