2 Mbiri 4:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 zozimitsira nyale, mbale zolowa, makapu, ndi zopalira moto. Zonsezi zinali zagolide woyenga bwino.+ Anapanganso khomo lolowera m’nyumbayo,+ zitseko zamkati za Chipinda Choyera Koposa, ndi zitseko+ za nyumbayo. Zonsezi zinali zagolide.
22 zozimitsira nyale, mbale zolowa, makapu, ndi zopalira moto. Zonsezi zinali zagolide woyenga bwino.+ Anapanganso khomo lolowera m’nyumbayo,+ zitseko zamkati za Chipinda Choyera Koposa, ndi zitseko+ za nyumbayo. Zonsezi zinali zagolide.