-
2 Mbiri 5:13Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
13 Tsopano anthu oimba malipenga ndi oimba pakamwa anayamba kuimba mogwirizana+ n’kumamveka ngati mawu amodzi otamanda ndi kuthokoza Yehova. Komanso anayamba kuimba+ ndi malipenga, zinganga, ndi zoimbira zina potamanda+ Yehova ndi mawu akuti, “chifukwa iye ndi wabwino,+ pakuti kukoma mtima kwake kosatha+ kudzakhala mpaka kalekale.” Kenako mtambo unadzaza nyumbayo,+ nyumba ya Yehova.+
-