2 Mbiri 5:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Chifukwa cha mtambowo,+ ansembewo analephera kupitiriza kutumikira, popeza ulemerero+ wa Yehova unadzaza nyumba ya Mulungu woona. 2 Mbiri Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 5:14 Nsanja ya Olonda,5/1/1994, tsa. 10
14 Chifukwa cha mtambowo,+ ansembewo analephera kupitiriza kutumikira, popeza ulemerero+ wa Yehova unadzaza nyumba ya Mulungu woona.