5 ‘Kuchokera tsiku limene ndinatulutsa anthu anga m’dziko la Iguputo, sindinasankhe mzinda m’mafuko onse a Isiraeli woti iwo amangeko nyumba ya dzina langa+ kuti likhale kumeneko, ndipo sindinasankhe munthu woti akhale mtsogoleri wa anthu anga Aisiraeli.+