2 Mbiri 7:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 ndipo anthu anga+ otchedwa ndi dzina langa+ akadzichepetsa+ n’kupemphera,+ n’kufunafuna nkhope yanga,+ n’kusiya njira zawo zoipa,+ ine ndidzamva ndili kumwamba+ n’kuwakhululukira tchimo lawo+ ndipo ndidzachiritsa dziko lawo.+ 2 Mbiri Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 7:14 Galamukani!,2/8/1994, tsa. 12
14 ndipo anthu anga+ otchedwa ndi dzina langa+ akadzichepetsa+ n’kupemphera,+ n’kufunafuna nkhope yanga,+ n’kusiya njira zawo zoipa,+ ine ndidzamva ndili kumwamba+ n’kuwakhululukira tchimo lawo+ ndipo ndidzachiritsa dziko lawo.+