2 Mbiri 9:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Pomalizira pake Solomo anagona pamodzi ndi makolo ake, ndipo anaikidwa m’manda mu Mzinda wa Davide bambo ake.+ Kenako mwana wake Rehobowamu,+ anayamba kulamulira m’malo mwake.+
31 Pomalizira pake Solomo anagona pamodzi ndi makolo ake, ndipo anaikidwa m’manda mu Mzinda wa Davide bambo ake.+ Kenako mwana wake Rehobowamu,+ anayamba kulamulira m’malo mwake.+