2 Mbiri 10:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Kenako Mfumu Rehobowamu inatumiza Hadoramu+ amene anali kuyang’anira anthu ogwira ntchito yokakamiza, koma ana a Isiraeli anam’ponya miyala+ n’kumupha. Komabe, Mfumu Rehobowamu inakwanitsa kukwera galeta lake n’kuthawira ku Yerusalemu.+
18 Kenako Mfumu Rehobowamu inatumiza Hadoramu+ amene anali kuyang’anira anthu ogwira ntchito yokakamiza, koma ana a Isiraeli anam’ponya miyala+ n’kumupha. Komabe, Mfumu Rehobowamu inakwanitsa kukwera galeta lake n’kuthawira ku Yerusalemu.+