2 Mbiri 14:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Pomalizira pake, Abiya anagona pamodzi ndi makolo ake,+ ndipo anamuika m’manda mu Mzinda wa Davide.+ Kenako Asa+ mwana wake anayamba kulamulira m’malo mwake. M’masiku ake, m’dzikolo munalibe chosokoneza chilichonse+ kwa zaka 10.
14 Pomalizira pake, Abiya anagona pamodzi ndi makolo ake,+ ndipo anamuika m’manda mu Mzinda wa Davide.+ Kenako Asa+ mwana wake anayamba kulamulira m’malo mwake. M’masiku ake, m’dzikolo munalibe chosokoneza chilichonse+ kwa zaka 10.