2 Mbiri 16:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 M’chaka cha 39 cha ulamuliro wa Asa, iye anadwala nthenda ya mapazi+ mpaka matendawo anakula kwambiri. Koma ngakhale pamene anali kudwala, iye anafunafuna ochiritsa+ osati Yehova.+ 2 Mbiri Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 16:12 Nsanja ya Olonda,8/15/2012, tsa. 10
12 M’chaka cha 39 cha ulamuliro wa Asa, iye anadwala nthenda ya mapazi+ mpaka matendawo anakula kwambiri. Koma ngakhale pamene anali kudwala, iye anafunafuna ochiritsa+ osati Yehova.+