2 Mbiri 21:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Koma Aedomu anapitirizabe kugalukira Yuda mpaka lero. Inalinso nthawi imeneyi pamene Libina+ anagalukira Yuda ndi kuchoka m’manja mwa Yehoramu chifukwa iye anali atasiya Yehova Mulungu wa makolo ake.+
10 Koma Aedomu anapitirizabe kugalukira Yuda mpaka lero. Inalinso nthawi imeneyi pamene Libina+ anagalukira Yuda ndi kuchoka m’manja mwa Yehoramu chifukwa iye anali atasiya Yehova Mulungu wa makolo ake.+