2 Mbiri 27:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Yotamu+ anali ndi zaka 25 pamene anayamba kulamulira, ndipo analamulira ku Yerusalemu zaka 16. Mayi ake dzina lawo linali Yerusa+ mwana wa Zadoki.
27 Yotamu+ anali ndi zaka 25 pamene anayamba kulamulira, ndipo analamulira ku Yerusalemu zaka 16. Mayi ake dzina lawo linali Yerusa+ mwana wa Zadoki.