2 Mbiri 32:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 anagwirizana ndi akalonga ake+ ndi amuna ake amphamvu kuti atseke akasupe a madzi amene anali kunja kwa mzindawo,+ choncho iwo anamuthandiza.
3 anagwirizana ndi akalonga ake+ ndi amuna ake amphamvu kuti atseke akasupe a madzi amene anali kunja kwa mzindawo,+ choncho iwo anamuthandiza.