2 Mbiri 33:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Pomalizira pake Manase anagona pamodzi ndi makolo ake,+ ndipo anamuika m’manda+ panyumba yake. Kenako Amoni+ mwana wake anayamba kulamulira m’malo mwake.
20 Pomalizira pake Manase anagona pamodzi ndi makolo ake,+ ndipo anamuika m’manda+ panyumba yake. Kenako Amoni+ mwana wake anayamba kulamulira m’malo mwake.