-
2 Mbiri 34:9Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
9 Iwo anapita kwa Hilikiya+ mkulu wa ansembe n’kukapereka ndalama zimene anthu anali kubweretsa kunyumba ya Mulungu, zimene Alevi omwe anali alonda a pakhomo,+ anatolera ku fuko la Manase,+ la Efuraimu,+ kwa Aisiraeli onse,+ kwa Ayuda onse, ku fuko la Benjamini, ndi kwa anthu onse okhala mu Yerusalemu.
-