2 Mbiri 34:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Chotero Hilikiya anauza Safani+ mlembi kuti: “Ndapeza buku la chilamulo m’nyumba ya Yehova!” Pamenepo Hilikiya anapereka bukulo kwa Safani.
15 Chotero Hilikiya anauza Safani+ mlembi kuti: “Ndapeza buku la chilamulo m’nyumba ya Yehova!” Pamenepo Hilikiya anapereka bukulo kwa Safani.