2 Mbiri 34:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Atatero, Yosiya anachotsa zonyansa zonse+ m’mayiko onse a ana a Isiraeli.+ Anachititsanso anthu onse amene anali mu Isiraeli kuti ayambe kutumikira Yehova Mulungu wawo. M’masiku ake onse, iwo sanasiye kutsatira Yehova Mulungu wa makolo awo.+ 2 Mbiri Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 34:33 Nsanja ya Olonda,12/1/2005, tsa. 21
33 Atatero, Yosiya anachotsa zonyansa zonse+ m’mayiko onse a ana a Isiraeli.+ Anachititsanso anthu onse amene anali mu Isiraeli kuti ayambe kutumikira Yehova Mulungu wawo. M’masiku ake onse, iwo sanasiye kutsatira Yehova Mulungu wa makolo awo.+